Elige una pista para reproducir
Cheo Meek
Ooh ooh!
Chinsapo
Mad beats
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white koma ndikuchoka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Nchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso
Chinsapo izakupanga chitsanzo
I pray to God my soul to keep
Kwa sumanje kwa Dzombe kukagula weed
Amandifila amandiwona pa screen
Or ndikayika drip ngat mfana wa teams
Koma ndachoka kwa Chinsapo
Komwe ma babe amagomera bado
Ngati samayaka amangofuna bundle
Gang yanga ma dentist izakuchotsa Mano
Chinsapo, Chinsapo
Chinsapo, Chinsapo
Chinsapo, Chinsapo, Chinsapo
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white koma ndikuchoka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Nchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso
Chinsapo izakupanga chitsanzo
Ndingotula ndima Gees
Bola trizer I got the keys
Ndipo Ukuziwa kale ndimakhala busy
Undihalla chama three mwina nditha kukhala free
Komabe ase ukuziwa sitinga chille
I gotta tell your straight ndisakubisile
I'm moving smart koma sindimapisila
And I'm talking shit koma sindinazipisire
Ndimamenyaso ma punch guys wina andigwire
Gist imandikhala ngati mpando
You can't walk in my shoes uzingovala sandals
Money talks mphwanga usachulutse nthano
Muka tinter ngati Spe musachulutse kano
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white koma ndikuchoka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Nchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso
Chinsapo izakupanga chitsanzo
Cheo Meek you've been killing it