Elige una pista para reproducir

Ay! Eh ay! Ay! Eh Ay!
Phone Five Mita nakuuza udzatenge
Rent Two Mita ubwela udzatenga
Koma suyamika, umanditenga opepela
Suyamika umanditenga opepela
Ndiphulila, ine zanga ndiphulila
Ndiphulila, ine zanga ndiphulila
Ukulila, kukusiya ukulila iwe!
Ukulila, kukusiya ukulila
Ndiphuli
Ine zanga ndiphulila
Ukuli
Kukusiya ukulila
Ndiphuli
Ine zanga ndiphulila
Ukuli
Kukusiya ukulila ah ah ah
Unalibe shoes ndagula folo pano uziti wathesa
Uwoneke dolo ine opusa ayi izo sizotheka
Ndinyamula! Kuli konse ukasume
Ndinyamuula kuli konse ukasumeee
Ndiphulila, ine zanga ndiphulila
Ndiphulila, ine zanga ndiphulila
Ukulila, kukusiya ukulila iwe!
Ukulila, kukusiya ukulila
Ndiphuli
Ine zanga ndiphulila
Ukuli
Kukusiya ukulila
Ndiphuli
Ine zanga ndiphulila
Ukuli
Kukusiya ukulila ah ah ah