Elige una pista para reproducir
Its Macia the rhythm boy
Iyakayaka yooh
Uuuooh Uuuuh
Misozi ndi chimwemwe
Anzanga ndaivala velo
Ndinkangosilila
Ali ndi ring pa chala
Tsiku langa lafika
Ndikuyamika ku mwamba
DJ kweza nyimbo
Deebo!
Ngati kutulo ndinkangiwa ku believer
Pa dzana paja ndinkafuna kugiver aah
Lelo ngati bodza ndili taken (Taken)
Pa altar kandilekeni (Lekeni)
Finally, ndapeza wanga andimale eee!
Ngati bodza ndili taken
Pa altar kandilekeni
Finally, ndapeza wanga andimale eee!
Misozi ndi chimwemwe
Anzanga ndaivala velo
Ndinkangosilila
Ali ndi ring pa chala
Tsiku langa lafika
Ndikuyamika kumwamba
DJ kweza nyimbo
Anzanga onse anatengedwa
Kungoshala ndekha
Mkumazifunsa, Yahweh ndinalakwa chani eeh
Body ndiyamushe ine eya!
Face ndiyamushe ine eya!
Koma ndilibe ring
Yeah man ndilibe ring
Oh mama yawe! Lelo wapanga za ine
Oh mama yawe! Inu wadalitsa ah ah!
Misozi ndi chimwemwe
Anzanga ndaivala velo
Ndinkangosilila
Ali ndi ring pa chala
Tsiku langa lafika
Ndikuyamika kumwamba
DJ kweza nyimbo
Ndi mkafuna onsambitsa (ooah!)
Ndi mkafuna onchengeta (ooha!)
Ndi mkafuna ondihoda (Iyakayaka yo)
Ndi mkafuna ondikonda
Ndi mkafuna onsambitsa (ooah!)
Ndi mkafuna onchengeta (ooha!)
Ndi mkafuna ondihoda (Iyakayaka yo)
Ndi mkafuna ondikonda
Misozi ndi chimwemwe
Anzanga ndaivala velo
Ndinkangosilila
Ali ndi ring pa chala
Tsiku langa lafika
Ndikuyamika kumwamba
DJ kweza nyimbo
Misozi ndi chimwemwe
Anzanga ndaivala velo
Ndinkangosilila
Ali ndi ring pa chala
Tsiku langa lafika
Ndikuyamika kumwamba
DJ kweza nyimbo