Оберіть трек для відтворення
Machesi ndayatsa but you're already on fire
Moto obadwa nawo amakutcha born fire
Nkhani ndi nkhani kodi zimatheka bwanji
Nditenge madzi mwina nkudzandi tentha
Kodi mayi, mayi
Mayi waona ndani
Mayi ukumwa chani
Mayi dzina ndi ndani
Kodi mayi, mayi
Mayi wabetcha ndani
Mayi ukumwa chani
Mayi dzina ndi ndani
Kodi mayi
Mayi waona ndani
Kodi mayi
Mayi dzina ndi ndani
Kodi mayi
Mayi
Ali bububu!
Nkazi ali bububu!
Lit nga chigububu
Chance ili ukuku ili ukuku
Size yangatu
Maine gwileni ndingafe
Nkazi mikanda ili mbwee
Chiwuno chofewa ngati bread
Ali diku diku ali peng yeah
Ali peng yeh
Ngati bread yeh
Akufewa yeah
Diku diku yeh
Diku diku yeh
Diku diku yeh
Diku diku yeh
Diku diku yeh